Aroma 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 omwe ndi Aisiraeli. Mulungu anawatenga kuti akhale ana ake+ ndipo anawapatsa ulemerero, mapangano,+ Chilamulo,+ utumiki wopatulika+ komanso malonjezo.+
4 omwe ndi Aisiraeli. Mulungu anawatenga kuti akhale ana ake+ ndipo anawapatsa ulemerero, mapangano,+ Chilamulo,+ utumiki wopatulika+ komanso malonjezo.+