Aroma 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+
7 Ndiponso sikuti onse ndi ana chifukwa choti ndi mbadwa* za Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.”+