Aroma 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lonjezolo silinaperekedwe pa nthawi iyi yokha. Linaperekedwanso pamene Rabeka ankayembekezera kubereka ana amapasa a Isaki kholo lathu lija.+
10 Lonjezolo silinaperekedwe pa nthawi iyi yokha. Linaperekedwanso pamene Rabeka ankayembekezera kubereka ana amapasa a Isaki kholo lathu lija.+