-
Aroma 9:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mapasawo asanabadwe ndiponso asanachite chabwino kapena choipa chilichonse, Mulungu anasonyeza kuti cholinga chake chidzadalira iye amene amaitana, osati zochita za munthu.
-