Aroma 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Ndinakonda Yakobo, koma Esau ndinadana naye.”+