Aroma 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi simukudziwa kuti woumba mbiya ali ndi ufulu woumba+ chinthu china cha ntchito yolemekezeka, china cha ntchito yonyozeka kuchokera pa dongo limodzi? Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:21 Nsanja ya Olonda,6/15/2013, ptsa. 25-262/1/1999, tsa. 10
21 Kodi simukudziwa kuti woumba mbiya ali ndi ufulu woumba+ chinthu china cha ntchito yolemekezeka, china cha ntchito yonyozeka kuchokera pa dongo limodzi?