Aroma 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso mogwirizana ndi zimene Yesaya ananeneratu, “Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba akanapanda kutisiyira mbadwa,* tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:29 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yesaya 1, ptsa. 20-21
29 Ndiponso mogwirizana ndi zimene Yesaya ananeneratu, “Yehova* wa magulu ankhondo akumwamba akanapanda kutisiyira mbadwa,* tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.”+