Aroma 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Inetu ndikuika mwala+ wopunthwitsa ndiponso thanthwe lokhumudwitsa mu Ziyoni, koma munthu wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”+
33 mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Inetu ndikuika mwala+ wopunthwitsa ndiponso thanthwe lokhumudwitsa mu Ziyoni, koma munthu wokhulupirira mwalawo sadzakhumudwa.”+