Aroma 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa ngati ukulengeza ‘mawu amene ali mʼkamwa mwakowo,’ akuti Yesu ndi Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa, udzapulumuka. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1997, tsa. 19
9 Chifukwa ngati ukulengeza ‘mawu amene ali mʼkamwa mwakowo,’ akuti Yesu ndi Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa, udzapulumuka.