Aroma 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Palibe kusiyana pakati pa Myuda ndi Mgiriki,+ popeza kwa onsewo Ambuye ndi mmodzi, amene amapereka mowolowa manja kwa onse oitana pa dzina lake. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:12 Nsanja ya Olonda,12/15/1997, tsa. 19
12 Palibe kusiyana pakati pa Myuda ndi Mgiriki,+ popeza kwa onsewo Ambuye ndi mmodzi, amene amapereka mowolowa manja kwa onse oitana pa dzina lake.