Aroma 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yesaya analankhula molimba mtima kwambiri kuti: “Anthu amene anandipeza ndi amene sankandifunafuna.+ Ndinadziwika kwa anthu amene sanafunse za ine.”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:20 Yesaya 2, tsa. 373
20 Koma Yesaya analankhula molimba mtima kwambiri kuti: “Anthu amene anandipeza ndi amene sankandifunafuna.+ Ndinadziwika kwa anthu amene sanafunse za ine.”+