Aroma 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye zili bwanji pamenepa? Chimene Aisiraeli akuchifunitsitsa sanachipeze, koma anthu osankhidwa ndi amene anachipeza.+ Enawo anaumitsa mitima yawo+
7 Ndiye zili bwanji pamenepa? Chimene Aisiraeli akuchifunitsitsa sanachipeze, koma anthu osankhidwa ndi amene anachipeza.+ Enawo anaumitsa mitima yawo+