Aroma 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ngati mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tofa nato,+ maso osaona ndi makutu osamva, mpaka lero.”+
8 ngati mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tofa nato,+ maso osaona ndi makutu osamva, mpaka lero.”+