Aroma 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwatu ngati dziko lagwirizanitsidwa ndi Mulungu chifukwa chakuti iwo anatayidwa,+ ndiye kuti akadzalandiridwa zidzakhala ngati awaukitsa.
15 Chifukwatu ngati dziko lagwirizanitsidwa ndi Mulungu chifukwa chakuti iwo anatayidwa,+ ndiye kuti akadzalandiridwa zidzakhala ngati awaukitsa.