-
Aroma 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ngati nthambi zina zinadulidwa, ndipo iwe ngakhale kuti ndiwe nthambi ya mtengo wa maolivi wamʼtchire, unalumikizidwa pakati pa nthambi zotsala ndipo unayamba kupeza zonse zofunika kuchokera ku muzu wamtengo wa maoliviwo,
-