Aroma 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 usayambe kukulira mtima nthambi zimene zinadulidwazo. Koma ngati ukuzikulira mtima+ kumbukira kuti si iwe amene ukunyamula muzu, koma muzu ndi umene ukukunyamula iweyo.
18 usayambe kukulira mtima nthambi zimene zinadulidwazo. Koma ngati ukuzikulira mtima+ kumbukira kuti si iwe amene ukunyamula muzu, koma muzu ndi umene ukukunyamula iweyo.