Aroma 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimenezo nʼzoona. Iwo anadulidwa chifukwa analibe chikhulupiriro,+ koma iweyo udakali wolumikizidwa kumtengowo chifukwa cha chikhulupiriro.+ Chotsa maganizo odzikuzawo, koma khala ndi mantha.
20 Zimenezo nʼzoona. Iwo anadulidwa chifukwa analibe chikhulupiriro,+ koma iweyo udakali wolumikizidwa kumtengowo chifukwa cha chikhulupiriro.+ Chotsa maganizo odzikuzawo, koma khala ndi mantha.