Aroma 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uziganizira kukoma mtima komanso kusalekerera kwa Mulungu.+ Amene anagwa anasonyezedwa kusalekerera,+ koma iweyo unasonyezedwa kukoma mtima kwa Mulungu. Bola ukhalebe woyenera kusonyezedwa kukoma mtima kwake. Apo ayi, iwenso udzadulidwa.
22 Uziganizira kukoma mtima komanso kusalekerera kwa Mulungu.+ Amene anagwa anasonyezedwa kusalekerera,+ koma iweyo unasonyezedwa kukoma mtima kwa Mulungu. Bola ukhalebe woyenera kusonyezedwa kukoma mtima kwake. Apo ayi, iwenso udzadulidwa.