-
Aroma 11:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ngati iweyo unadulidwa kumtengo wa maolivi umene mwachilengedwe umamera mʼtchire, ndipo mosemphana ndi chilengedwe unalumikizidwa kumtengo wa maolivi wolimidwa, kodi si chapafupi kulumikiza nthambizi kumtengo wawo umene zinadulidwako?
-