Aroma 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nʼzoona kuti iwo ndi adani a uthenga wabwino ndipo zimenezi zakuthandizani inuyo. Koma Mulungu anawasankha ndipo amawakonda chifukwa cha makolo awo akale.+
28 Nʼzoona kuti iwo ndi adani a uthenga wabwino ndipo zimenezi zakuthandizani inuyo. Koma Mulungu anawasankha ndipo amawakonda chifukwa cha makolo awo akale.+