-
Aroma 11:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Mulungu sadzanongʼoneza bondo chifukwa cha mphatso zake ndiponso chifukwa chakuti anawaitana.