Aroma 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tili ndi mphatso zosiyanasiyana mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu kumene tinasonyezedwa.+ Choncho kaya tili ndi mphatso ya ulosi, tiyeni tizilosera mogwirizana ndi chikhulupiriro chathu. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 24-25 Nsanja ya Olonda,10/15/2009, tsa. 3
6 Tili ndi mphatso zosiyanasiyana mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu kumene tinasonyezedwa.+ Choncho kaya tili ndi mphatso ya ulosi, tiyeni tizilosera mogwirizana ndi chikhulupiriro chathu.