-
Aroma 13:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Nʼchifukwa chake mumakhomanso misonkho, popeza iwo ndi antchito a Mulungu otumikira anthu ndipo akukwaniritsa cholinga chimenechi nthawi zonse.
-