Aroma 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wina amaona tsiku lina ngati loposa linzake,+ koma wina amaona kuti masiku onse ndi ofanana.+ Munthu aliyense azitsimikiza kuti zimene akukhulupirira nʼzolondola. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:5 Nsanja ya Olonda,2/1/2010, tsa. 149/1/2004, ptsa. 9-10
5 Wina amaona tsiku lina ngati loposa linzake,+ koma wina amaona kuti masiku onse ndi ofanana.+ Munthu aliyense azitsimikiza kuti zimene akukhulupirira nʼzolondola.