Aroma 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tikakhala ndi moyo, timakhalira moyo Yehova,*+ ndipo tikafa, timafera Yehova.* Choncho kaya tikhale ndi moyo kapena tife, ndife a Yehova.*+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:8 Nsanja ya Olonda,11/1/2002, tsa. 152/1/1986, tsa. 10
8 Tikakhala ndi moyo, timakhalira moyo Yehova,*+ ndipo tikafa, timafera Yehova.* Choncho kaya tikhale ndi moyo kapena tife, ndife a Yehova.*+