Aroma 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 35 Nsanja ya Olonda,9/1/2004, tsa. 10
10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+