Aroma 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiye tisamaweruzane,+ koma mʼmalomwake tsimikizani mtima kuti simukuchita chilichonse chimene chingakhumudwitse kapena kupunthwitsa mʼbale wanu.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:13 Galamukani!,10/8/2005, tsa. 17
13 Ndiye tisamaweruzane,+ koma mʼmalomwake tsimikizani mtima kuti simukuchita chilichonse chimene chingakhumudwitse kapena kupunthwitsa mʼbale wanu.+