Aroma 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikudziwa ndipo ndikukhulupirira mwa Ambuye Yesu kuti palibe chakudya chimene pachokha ndi chodetsedwa.+ Koma ngati munthu akuona kuti chinachake nʼchodetsedwa, kwa iyeyo ndi chodetsedwa.
14 Ndikudziwa ndipo ndikukhulupirira mwa Ambuye Yesu kuti palibe chakudya chimene pachokha ndi chodetsedwa.+ Koma ngati munthu akuona kuti chinachake nʼchodetsedwa, kwa iyeyo ndi chodetsedwa.