Aroma 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa ngati mʼbale wanu akukhumudwa chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukusonyezanso chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera chifukwa cha zakudya zanu.+
15 Chifukwa ngati mʼbale wanu akukhumudwa chifukwa cha chakudya, ndiye kuti simukusonyezanso chikondi.+ Musawononge* munthu amene Khristu anamufera chifukwa cha zakudya zanu.+