Aroma 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa pa nkhani ya Ufumu wa Mulungu chofunika kwambiri si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo, mtendere ndi chimwemwe zimene zimabwera ndi mzimu woyera. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:17 Nsanja ya Olonda,6/15/2008, tsa. 31
17 Chifukwa pa nkhani ya Ufumu wa Mulungu chofunika kwambiri si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo, mtendere ndi chimwemwe zimene zimabwera ndi mzimu woyera.