Aroma 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Siyani kuwononga ntchito ya Mulungu chifukwa cha zakudya basi.+ Zoonadi, zinthu zonse nʼzoyera, koma nʼkulakwa kudya zinthuzo ngati wina akukhumudwa nazo.+
20 Siyani kuwononga ntchito ya Mulungu chifukwa cha zakudya basi.+ Zoonadi, zinthu zonse nʼzoyera, koma nʼkulakwa kudya zinthuzo ngati wina akukhumudwa nazo.+