-
Aroma 14:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Chikhulupiriro chimene uli nacho, ukhale nacho pakati pa iweyo ndi Mulungu. Munthu amakhala wosangalala ngati sakudziimba mlandu pa zinthu zimene wasankha.
-