-
Aroma 14:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma ngati akudya kwinaku akukayikira, ameneyo watsutsidwa kale, chifukwa sakudya mogwirizana ndi chikhulupiriro. Ndithu, chilichonse chochitidwa mosemphana ndi chikhulupiriro ndi tchimo.
-