Aroma 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kunena zoona, Khristu anakhala mtumiki wa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika posonyeza kuti malonjezo amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika.+
8 Kunena zoona, Khristu anakhala mtumiki wa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika posonyeza kuti malonjezo amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika.+