Aroma 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ winawake amene adzatuluke kuti alamulire mitundu.+ Chiyembekezo cha anthu a mitundu ina chidzakhala pa iyeyo.”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:12 Nsanja ya Olonda,10/1/2008, ptsa. 4-5
12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ winawake amene adzatuluke kuti alamulire mitundu.+ Chiyembekezo cha anthu a mitundu ina chidzakhala pa iyeyo.”+