-
Aroma 15:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Anandisonyeza kukoma mtima kumeneku kuti ndigwire ntchito yolengeza uthenga wabwino wa Mulungu monga wantchito wa Khristu Yesu, wotumikira anthu a mitundu ina.+ Ndikugwira ntchito yopatulikayi kuti anthu a mitundu inawa akhale ngati nsembe yovomerezeka kwa Mulungu+ imene yayeretsedwa ndi mzimu woyera.
-