-
Aroma 15:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Sindidzalankhula chilichonse chimene ndachita pandekha, koma zokhazo zimene Khristu wachita ndi kulankhula kudzera mwa ine kuti ndithandize anthu a mitundu ina kukhala omvera.
-