-
Aroma 15:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pochita zimenezi ndinatsimikiza mtima kuti ndisalengeze uthenga wabwino kumene anthu ankadziwa kale za Khristu nʼcholinga choti ndisamange pamaziko a munthu wina,
-