Aroma 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma tsopano kulibenso gawo limene sindinafikeko mʼmadera amenewa, ndipo kwa zaka zambiri* ndakhala ndikulakalaka kufika kwanuko. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2020, ptsa. 16-17
23 Koma tsopano kulibenso gawo limene sindinafikeko mʼmadera amenewa, ndipo kwa zaka zambiri* ndakhala ndikulakalaka kufika kwanuko.