-
Aroma 15:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Choncho ndili ndi chikhulupiriro kuti ndikamadzapita ku Sipaniya ndidzaonana nanu ndipo ndikadzacheza nanu kwakanthawi, mudzandiperekeza pa ulendo wangawo.
-