Aroma 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Abale a ku Makedoniya ndi a ku Akaya apereka mosangalala mphatso kwa oyera ena a ku Yerusalemu omwe ndi osauka.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:26 Nsanja ya Olonda,10/15/1986, tsa. 23
26 Abale a ku Makedoniya ndi a ku Akaya apereka mosangalala mphatso kwa oyera ena a ku Yerusalemu omwe ndi osauka.+