1 Akorinto 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi Khristu wakhala wogawanika? Kodi Paulo anapachikidwa pamtengo wozunzikirapo* kuti inu mupulumutsidwe? Kapena kodi munabatizidwa mʼdzina la Paulo?
13 Kodi Khristu wakhala wogawanika? Kodi Paulo anapachikidwa pamtengo wozunzikirapo* kuti inu mupulumutsidwe? Kapena kodi munabatizidwa mʼdzina la Paulo?