1 Akorinto 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhani yokhudza mtengo wozunzikirapowo* ndi chinthu chopusa kwa anthu amene akupita kukawonongedwa,+ koma kwa ife amene tikupulumutsidwa, imeneyi ndi mphamvu ya Mulungu.+
18 Nkhani yokhudza mtengo wozunzikirapowo* ndi chinthu chopusa kwa anthu amene akupita kukawonongedwa,+ koma kwa ife amene tikupulumutsidwa, imeneyi ndi mphamvu ya Mulungu.+