1 Akorinto 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi wanzeru ali kuti? Mlembi* ali kuti? Katswiri wa mtsutso wa nthawi* ino ali kuti? Kodi Mulungu sanapange nzeru zadzikoli kukhala zopusa? 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1992, ptsa. 19-20 Kukambitsirana, tsa. 139
20 Kodi wanzeru ali kuti? Mlembi* ali kuti? Katswiri wa mtsutso wa nthawi* ino ali kuti? Kodi Mulungu sanapange nzeru zadzikoli kukhala zopusa?