1 Akorinto 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu anasankhanso zinthu zonyozeka za dziko ndi zinthu zimene anthu amaziona ngati zachabechabe, zinthu zimene palibe, kuti achititse zinthu zimene zilipo kukhala zopanda mphamvu.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:28 Nsanja ya Olonda,7/1/1988, ptsa. 28-29
28 Mulungu anasankhanso zinthu zonyozeka za dziko ndi zinthu zimene anthu amaziona ngati zachabechabe, zinthu zimene palibe, kuti achititse zinthu zimene zilipo kukhala zopanda mphamvu.+