-
1 Akorinto 2:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe maganizo a munthu wina? Aliyense amangodziwa zimene zili mumtima mwake basi. Mofanana ndi zimenezi, palibe amene akudziwa maganizo a Mulungu, kupatulapo mzimu wa Mulungu.
-