1 Akorinto 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinakupatsani mkaka, osati chakudya chotafuna, chifukwa munali musanalimbe mokwanira. Ndipo mpaka pano simunalimbebe,+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, tsa. 29
2 Ndinakupatsani mkaka, osati chakudya chotafuna, chifukwa munali musanalimbe mokwanira. Ndipo mpaka pano simunalimbebe,+