1 Akorinto 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 chifukwa mukuganizabe ngati anthu amʼdzikoli.*+ Nanga ngati mukuchitirana nsanje ndiponso kukangana nokhanokha, si ndiye kuti ndinu akuthupi+ ndipo mukuyenda ngati anthu a mʼdzikoli? 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,3/1/1991, ptsa. 21-22
3 chifukwa mukuganizabe ngati anthu amʼdzikoli.*+ Nanga ngati mukuchitirana nsanje ndiponso kukangana nokhanokha, si ndiye kuti ndinu akuthupi+ ndipo mukuyenda ngati anthu a mʼdzikoli?