1 Akorinto 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi Apolo ndi ndani? Nanga Paulo ndi ndani? Ife tangokhala atumiki+ amene tinakuthandizani kukhala okhulupirira, mogwirizana ndi ntchito imene Ambuye anatipatsa.
5 Kodi Apolo ndi ndani? Nanga Paulo ndi ndani? Ife tangokhala atumiki+ amene tinakuthandizani kukhala okhulupirira, mogwirizana ndi ntchito imene Ambuye anatipatsa.