1 Akorinto 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho wofunika kwambiri si amene anadzala kapena amene anathirira, koma Mulungu amene amakulitsa.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, ptsa. 12, 163/1/1993, ptsa. 20-23
7 Choncho wofunika kwambiri si amene anadzala kapena amene anathirira, koma Mulungu amene amakulitsa.+